Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

70. Tidzaima Bwanji Pa Chiweruzo?

WHEN JESUS SHALL GATHER

WHEN JESUS SHALL GATHER

1. Mmene Yesu adzasonkhatu, Mitundu yonse ya dziko,
Kodi tidzaima bwanji’fe Pa mpando wachiweruzo?

* CHORUS:
Adzasonkhanitsa tiriguyo, Koma mankhusu adzataya;
Nanga tidzaima bwanji ko’ Pa tsiku la chiweruzo?
*
2. Kodi tidzamva mau ake, Wachita bwino iwetu,
Kapena tidzanjenjemera, Tidzachotsedwa ku mpando?

3. Iye adzakondwera ndithu, Kuona owomboledwa,
Adzawabvekatu zobvala, Pa kugwadira Mbuyeyo.

4. Tiyeni tidikire tsono, Ndi nyali zathu zowala,
Poitana Mkwati ku phwando Tidzakhale okonzeka.

5. Tikakhala okonzekatu, Tikakhala opirira;
Podzatha ulendo wathuwu, Tidzanka naye kumwamba.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 70

Permanent page: number and title URL

This page preserves Tidzaima Bwanji Pa Chiweruzo? as Hymn 70 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.