Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
71. Kodi Dzina Langa Lalembedwamo?
IS MY NAME WRITTEN THERE?
IS MY NAME WRITTEN THERE?
1. Mbuye sindisamala kukhala wachuma;
Ndifuna kukalowa m’dziko la kumwamba;
M’bukhu lokometsetsa la ufumu wanu,
Kodi lalembedwamo Mbuye dzina langa.
* CHORUS:
Kodi dzina langa, Lalembedwa m’mwamba?
M’bukhu la ufumuwo, Kodi lalembedwa?
*
2. Machimo anga alipo ambiri-mbiri,
Koma mwazi wa Mpulumutsi wandikwana;
Chifukwa lonjezano lanu lilipobe,
Ngakhale afiire, ndidzawayeretsa.
3. Ku mzinda wokoma wa malo owala’wo
Ndi anthu ovala za ulemelerozo;
Kumene choipa sichidzaonongako,
Kodi dzina langali lilipo m’bukhumo?
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 71
Permanent page: number and title URL
This page preserves Kodi Dzina Langa Lalembedwamo? as Hymn 71 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.