Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

74. M’mawa Tidzafesa

SOWING IN THE MORNING

SOWING IN THE MORNING

1. M’mawa tidzafesa mbeu zakukoma,
Msana ndi usiku tidzafesanso,
Nyengo ya masika tidzatema m’munda
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

*CHORUS:
Ndi zipatsozo, ndi zipatsozo
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.
*

2. Tidzifesa m’dzuwa tidzifesa m’thunzi,
Sitiopa ife mtambo ndi mphepo.
Athatu masika nchitozi zidzatha,
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

3. Tingolira kaya koma tidzafesa
Mbeu za Ambuye ntchito ya Yesu.
Adzachotsa msozi adzatilandira,
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 74

Permanent page: number and title URL

This page preserves M’mawa Tidzafesa as Hymn 74 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.