Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

76. Ndikonda Kuuzabe

I LOVE TO TELL THE STORY

I LOVE TO TELL THE STORY

1. Ndikonda kuuzabe, nthano ya Yesu, ndi
Zosaoneka zomwe, za m’mwamba zakezi;
Ndikonda kuuzabe, za cikondi chake,
Kubukitsa mbiriyo ya Mwana wa Mlungu.

* CHORUS:
Ndikonda kuuzabe, za Yesu mwini wanga,
Za chifundo chakecho, Ndiyimbe kumwamba.
*
2. Ndikonda kuuzabe, nthano yozizwitsa
Chifukwa ipambana, zonse zina ndamva;
Ndikonda kuuzabe, zomwe achitira
Kwa ine ndi kwa onse, a m’mvera ndi mtima.

3. Ndikonda kuuzabe, nthano yokomayo
Nthawi zonse ndiyimva, ndisekereranso.
Ndifuna kuuzabe kumvetsa amene
Sanamve za Mulungu, Wopulumutsayo.

4. Ndikonda kuuzabe, Mpulumutsi wanga
Natsika kumwambako natifera dala
Nakweranso kwawoko nadzadzanso Iye,
Kusonkhanitsa ake, Naye kukhalabe.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 76

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndikonda Kuuzabe as Hymn 76 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.