Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

78. Kupulumutsa Omwe Ali Kufa

RESCUE THE PERISHING

RESCUE THE PERISHING

1. Pulumutsa omwe ali kufatu,
Uwachotse m’manda a uchimo;
Lilira ochimwa, nuwadzutsetu,
Nuwauze za Yesu Mbuyeyo.*
*

*CHORUS:
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.*

2. Ngakhale amkana, Iye alinda,
Afuna kulandira olapa.
Awapembedzera moona Mtima,
Adzawakhululukira iwo.

3. Mu Mtima wa munthu muli zambiri,
Koma Yesu azichotsa zonse;
Atakhudzidwa ndi chikondi chake,
Nsinga za Satana zidzaduka.

4. Pulumutsa omwe ali kufatu
Limbitsa othodwa ndi olema;
Kwabwezera m’njira yopapatiza,
Ndi kuwauza za Mpulumutsi

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 78

Permanent page: number and title URL

This page preserves Kupulumutsa Omwe Ali Kufa as Hymn 78 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.