Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

92. Msaiwale Tsiku La Mbuye

DON’T FORGET THE SABBATH

DON’T FORGET THE SABBATH

1. Msaiwale tsiku la Mbuye wathuyo.
Ndi tsiku lopambana masiku enawo;
Ndi tsiku lakupuma ndi la chimwemwecho,
Kuwala kwake kuli kochoka mmwambamo.*
*

*CHORUS:
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.*

2. Sunga tsiku lake lopatulikalo,
Pembedza mwini njira yakunka mmwambamo;
Tikamtsatira Iye pa dziko linotu,
Adzatipatsa madzi a moyo wakewo.

3. Timyimbira Yesu pa tsiku lonseli,
Ambuye ali Bwenzi la ana onsewo.
Wokoma mtima ndinu, Mukhale nafetu,
Munalonjeza kuti mudzadza m’mtimamu.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 92

Permanent page: number and title URL

This page preserves Msaiwale Tsiku La Mbuye as Hymn 92 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.