Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

93. Sabata Nla Kupuma

O DAY OF REST AND GLADNESS

O DAY OF REST AND GLADNESS

1. Sabata nla kupuma, Ndi la chimwemwecho,
Ndi tsiku lotonthoza, Lokometsetsatu;
Akulu ndi ang’ono, Tigwade tonsefe,
Tiyimbe kwa Woyera Wa nthawi zonsezo.

2. Sabata lili ngati Chotchinjiriza ’fe,
Ndi monga ngati munda Wotupa mdambomo;
Litsitsimutsa m’yoyo Ya akutopawo,
Popuma pa Sabata Tiona mwambamo.

3. Ndi tsiku lakusinkha, Ndi la chikondicho,
Lakuyanjana nazo Za mwambamwambamo;
Tipeze zakukoma Zoposa zinazo,
Tifuna kupumula Kosatha mwambamo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 93

Permanent page: number and title URL

This page preserves Sabata Nla Kupuma as Hymn 93 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.