Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
232. Sindidzakusiya
I WILL NEVER LEAVE THEE
I WILL NEVER LEAVE THEE
1. Sindidzakusiya konse, Sindidzakukananso;
Ndzatsogola ndzakusunga, Mongwa mwa dzina langa;
Musaope coipaco, pomvera malangizo.
2. Mphepo zikaomba mkuntho, upemphere kwa Ine;
Ndidzakufungata iwe, Kukusamala bwino;
Poyesedwa konyazitsa, Ndidzakuyendetsa bwino.
3. Mlengalenga pong’azima pakakoma ponsepo,
Madyerero osasowa, Zokondweretsa zokha;
Ndidzakhala nawe ndithu, Ndi kuti usacimwe.
4. Ngati ndadodometsedwa, Ndi nkhawa ndi cisoni,
Ngakhaletu kuli nkhungu, Ndidzakuunikira,
Mbendera yokwezekayi, Ya cikondi canga njo.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 232
Permanent page: number and title URL
This page preserves Sindidzakusiya as Hymn 232 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.