Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
39. Thanthwe Lolimba
MY HOPE IS BUILT
MY HOPE IS BUILT
1. Chiyembekezo changatu, Chili mwa Yesu Woyera
Sindikhulupira wina Koma dzina la Yesuyo.
*CHORUS:
Ndaima pa Khristu Thanthwe, Nthaka yonse ndiyo mchenga,
Nthaka yonse ndiyo mchenga.*
2. Pondiphimba ine mdima, Ndipumula mwa Iyeyo,
M’namondwe ndi m’mphepo zonse, Ndithawira kwa Iyeyo.
3. Pangano lake ndi mwazi, Zinditchinjiriza ine,
Ndikalepheratu pena, Ndidzakhalatu mwa Iye.
4. Pamene Iye adzadza, Ndidzapezeke mwa Iye,
Ndiri m’chilungamo chake, Wopanda naye chifukwa.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 39
Permanent page: number and title URL
This page preserves Thanthwe Lolimba as Hymn 39 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.